Onerani, mverani ndi kutsitsa/dawuniloda mapulogalamu a maphunizilo othandiza pa nkani ya mphamvu mu dela lanu
Pulogalamu ya Pansasa
Pulogalamu ya Mr Magetsi and Mrs Makala ili pansi pa mapulogalamu ophunzitsa za mphamvu. Pansasa, inaulutsidwa ndi likulu la mabungwe omwe ankagwila ntchinto za SE4ALL muno mu Malawa. Mvelani mapulogalamu a Pansasa.