YOUR COMMUNITY'S PRACTICAL STUFFS
THE ENERGY POVERTY
previous arrow
next arrow
Slider

Mphamvu Now ndi kampeni yomwe ikuchitika pansi pa ndondomeko za mgwirizano wa njira zamakono za mphamvu zotchedwa Green and Inclusive Energy (GIE) motsogoleredwa ndi mabungwe asanu omwe si aboma. Cholinga cha Mphamvu Now ndi kugawa mautenga olondora pankani ya vuto la umphawi wa mphamvu mudziko lathu kupatikiza njila zothandiza kuthetsa vutoli ndi kuphunzitsa aMalawi njira zamakono zosiyana siyana zogwiritsa ntchinto mphamvu zosaononga chilengedwe ndinjila zolumikizana ndi aboma kuti achitepo kanthu pa nkani ya Green and Inclusive Energy.

 Mphamvu Now ikufuna kukwaniritsa zolinga zitatu izi;

Kukhazikitsa malo a dijito omwe ndiosavuta kugwiritsa kugwiritsa ntchito pophunzitsa mabungwe, madera komanso anthu za mphamvu

Kulimbikitsa a Malawi m’makomo mwao kuti adziwe komanso kuchitapo kanthu pa nkhani zokhudza mphamvu zosaononga chilengedwe

Kuthandiza kuti zolankhula zokhudza mphamvu zikhale zosavuta kumva kwa a Malawi komanso kuti zikhale mu ziyankhulo za ku Malawi konkuno

Upangiri wodalirika wa dera lanu!

Tili ndi nkhokwe ya zipangizo zomwe zingakuthandizeni kumvetsetsa kwanu kwa malamulo oyendetsera mphamvu kuno Ku Malawi, komanso zipangizo ndi malipoti Omwe mungafune

Nkhani Zatsopano

Understanding Messages On Our Roadside & Streetpole Billboards

Understanding Messages On Our Roadside & Streetpole Billboards

We are more than excited to announce that the roadside and street poles billboards have been erected in all cities and some district in North and Central regions! This has been done as part of a nationwide advocacy campaign on Green and Inclusive Energy (GIE). The team at Renew’N’Able Malawi tried to convey the messages […]
Community Energy Malawi Trains Development Workers

Community Energy Malawi Trains Development Workers

Community Energy Malawi (CEM), with support from Hivos, is implementing a project called Malawi for Green, Localised Inclusive and Decentralised Energy (Malawi GLIDE) in Balaka, Chitipa and Ntchisi districts. The Project aims at facilitating the mainstreaming of energy in the decentralized development planning and implementation processes as one way of building community awareness and capacity […]