YOUR COMMUNITY'S PRACTICAL STUFFS
THE ENERGY POVERTY
previous arrow
next arrow
Slider

Mphamvu Now ndi kampeni yomwe ikuchitika pansi pa ndondomeko za mgwirizano wa njira zamakono za mphamvu zotchedwa Green and Inclusive Energy (GIE) motsogoleredwa ndi mabungwe asanu omwe si aboma. Cholinga cha Mphamvu Now ndi kugawa mautenga olondora pankani ya vuto la umphawi wa mphamvu mudziko lathu kupatikiza njila zothandiza kuthetsa vutoli ndi kuphunzitsa aMalawi njira zamakono zosiyana siyana zogwiritsa ntchinto mphamvu zosaononga chilengedwe ndinjila zolumikizana ndi aboma kuti achitepo kanthu pa nkani ya Green and Inclusive Energy.

 Mphamvu Now ikufuna kukwaniritsa zolinga zitatu izi;

Kukhazikitsa malo a dijito omwe ndiosavuta kugwiritsa kugwiritsa ntchito pophunzitsa mabungwe, madera komanso anthu za mphamvu

Kulimbikitsa a Malawi m’makomo mwao kuti adziwe komanso kuchitapo kanthu pa nkhani zokhudza mphamvu zosaononga chilengedwe

Kuthandiza kuti zolankhula zokhudza mphamvu zikhale zosavuta kumva kwa a Malawi komanso kuti zikhale mu ziyankhulo za ku Malawi konkuno

Upangiri wodalirika wa dera lanu!

Tili ndi nkhokwe ya zipangizo zomwe zingakuthandizeni kumvetsetsa kwanu kwa malamulo oyendetsera mphamvu kuno Ku Malawi, komanso zipangizo ndi malipoti Omwe mungafune

Nkhani Zatsopano

Sports Bonanza ya GIE Yayambika!!!

Sports Bonanza ya GIE Yayambika!!!

Report by Caroline Kachipapa,edited by Kenneth Mtago Ngati njira imodzi yofalitsira uthenga wokhudza kasamalidwe ka chilengedwe komanso kumemeza anthu kugwiritsa ntchito mphamvu ya m’bwezera, bungwe la Renew’N’Able Malawi (RENAMA) likuchititsa masewero ampira wa miyendo komanso wamanja pakati pa sukulu za sekondale zokwana zisanu ndi zitatu m’madera a Lunzu komanso Chileka mu mzinda wa Blantyre. Masewerawa, […]
Renew’N’Able Malawi and Youth and Net Counselling Conducts a Joint Radio Program

Renew’N’Able Malawi and Youth and Net Counselling Conducts a Joint Radio Program

Renew’N’Able Malawi Advocacy and Communications Officer on Green and Inclusive Energy on MPHAMVU ZA CHILENGEDWE program with YONECO FM, hosted by Jonas Kachikho. The program was specially created for the project which aims at advocating for renewable energy in Malawi.
Green Inclusive Energy Excites District Health Office in Chitipa

Green Inclusive Energy Excites District Health Office in Chitipa

The Chitipa District Health Office (DHO) in Malawi is excited with the Green Inclusive Energy (GIE) project which Community Energy Malawi (CEM) is implementing in the district. The DHO lamented at the lack of technical backstopping on solar PV and other renewable energy systems installed at health centres in the district. “We have several partners […]